Kumene Tingapite Kuti?

Ndinakulira m'banja la Mboni za Yehova. Ndinkachita utumiki wa nthawi zonse m'maiko atatu, ndinkagwira ntchito limodzi ndi ma Beteli awiri, ndipo ndinathandiza ambiri mpaka kufika pobatizika. Ndinkanyadira kwambiri kunena kuti "ndili m'choonadi." Ndimakhulupilira kuti ndili mu ...