Kodi Muli M'pangano Latsopano?

(Yeremiya 31:33, 34). . “Pakuti ili ndi pangano ndidzapangana ndi nyumba ya Israyeli pambuyo pa masiku awo, ati Yehova. “Ndidzaika chilamulo changa mkati mwawo, ndipo ndidzachilemba mumtima mwawo. Ndipo ndidzakhala Mulungu wawo, ndi iwonso ....